Panthawi yina, kunali n’gona yanjala kwambili.
Once there was a very hungry crocodile.
Inasakila cakudya mosafulumila ndi mwacetecete. Kenako…
He searched for food slowly and quietly. And then…
Phoo!!! Ng’ona inagwila!
POW!!! The crocodile strikes!
Kucokela apo njala inasila, ndiponso ali osangalala.
After that he is no longer hungry, and he is happy.
Mpaka akakhalenso ndi njala.
Until he gets hungry again.