Tom amanyamula nswanda.
Tom carries a tray of ripe bananas.
Tom amapita ku msika kukagulisa nthochi.
Tom goes to the market to sell bananas.
Anthu pa msika agula ziphatso.
People at the market are buying fruit.
Koma palibe amene agula nthoci za Tom. Asankha kugula zipatso za azimai.
But no one is buying
Tom’s bananas.
They prefer to buy fruit from women.
“M’mudzi mwathu, azimai okha ndio amene agulitsa nthochi,” anthu amatero. “Kodi uyu ndi mwamuna wotani?” Anthu afunsa.
“In our community, only women sell fruit,” people say. “What kind of a man is this?” people ask.
Koma Tom saleka. Apunda, “Gulani nthoci zanga! Gulani nthoci zanga zakupsya komanso zonzuna”
But Tom does not give up.
He calls, “Buy my bananas!
Buy my sweet ripe bananas!”
Mkazi umozi atengapo nthochi zogula. Ayanganitsitsa nthoci mwacidwi.
One woman picks up a bunch of bananas from the tray.
She looks at the bananas carefully.
Mzimai agula ntochi.
The woman buys the bananas.
Anthu ambiri abwera kusitolo. Agula nthoci za Tom ndi kuzidya.
More people come to the stall.
They buy Tom’s bananas and eat them.
Posacedwa, zonse zatha. Tom awerengera ndalama zomwe wapanga.
Soon, the tray is empty.
Tom counts the money he earned.
Pambuyo pake, Tom agula sopo, shuga, ndi mkhate. Aika zinthu mu nswanda yake.
Then Tom buys soap, sugar, and bread.
He puts the things in his tray.
Tom waika nswanda yake pa mutu ndipo apita ku nyumba.
Tom balances the tray on his head and goes home.